Yeremiya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+
3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+