Yeremiya 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa amene adzaziwete moyenerera.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kuchita mantha ndipo palibe imene idzasowe,” akutero Yehova. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:4 Yeremiya, ptsa. 129-130
4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa amene adzaziwete moyenerera.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kuchita mantha ndipo palibe imene idzasowe,” akutero Yehova.