Yeremiya 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Koma masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene sadzalumbiranso kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa Aisiraeli mʼdziko la Iguputo.’+
7 “Koma masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene sadzalumbiranso kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa Aisiraeli mʼdziko la Iguputo.’+