-
Yeremiya 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndi ndani amene waimirira pagulu la anthu amene Yehova amawakonda
Kuti azindikire ndi kumva mawu ake?
Ndi ndani amene watchera khutu kuti amvetsere mawu ake?
-