-
Yeremiya 23:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Yehova wanena kuti: “Kodi ine ndimakhala Mulungu pamene ndili pafupi basi, osati pamenenso ndili patali?”