Yeremiya 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi maganizo onena zabodza apitiriza kukhala mumtima mwa aneneriwa mpaka liti? Iwo ndi aneneri amene amanena chinyengo chochokera mumtima mwawo.+
26 Kodi maganizo onena zabodza apitiriza kukhala mumtima mwa aneneriwa mpaka liti? Iwo ndi aneneri amene amanena chinyengo chochokera mumtima mwawo.+