Yeremiya 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo akufuna kuchititsa kuti anthu anga aiwale dzina langa pogwiritsa ntchito maloto amene aneneriwo amauzana, mofanana ndi mmene makolo awo anaiwalira dzina langa chifukwa cha Baala.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2019, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 10
27 Iwo akufuna kuchititsa kuti anthu anga aiwale dzina langa pogwiritsa ntchito maloto amene aneneriwo amauzana, mofanana ndi mmene makolo awo anaiwalira dzina langa chifukwa cha Baala.+