Yeremiya 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Ndipo anthu awa komanso mneneri kapena wansembe akakufunsa kuti, ‘Kodi uthenga* wa Yehova ukuti chiyani?’ uwayankhe kuti, ‘“Anthu inu ndinu katundu wolemera! Ndipo ndidzakutayani,”+ akutero Yehova.’ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:33 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 113/1/1994, tsa. 12
33 “Ndipo anthu awa komanso mneneri kapena wansembe akakufunsa kuti, ‘Kodi uthenga* wa Yehova ukuti chiyani?’ uwayankhe kuti, ‘“Anthu inu ndinu katundu wolemera! Ndipo ndidzakutayani,”+ akutero Yehova.’