-
Yeremiya 23:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Mneneri, wansembe kapena aliyense amene akunena kuti, ‘Uthenga uwu ndi katundu wolemera wa Yehova!’ ndidzalanga munthuyo ndi anthu a mʼnyumba yake.
-