-
Yeremiya 23:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Aliyense wa inu akufunsa mnzake ndi mʼbale wake kuti, ‘Kodi Yehova wayankha kuti chiyani? Ndipo Yehova wanena kuti chiyani?’
-