-
Yeremiya 23:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Koma musanenenso kuti uthenga wa Yehova ndi katundu wolemera, chifukwa katundu wolemera ndi mawu a aliyense wa inu ndipo mwasintha mawu a Mulungu wathu wamoyo, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-