-
Yeremiya 23:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Mukapitiriza kunena kuti, “Uthenga uwu ndi katundu wolemera wa Yehova!” Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti mukunenabe kuti, ‘Mawu a Yehova ndi katundu wolemera,’ ngakhale kuti ndinakuuzani kuti ‘Musamanene kuti: “Mawu a Yehova ndi katundu wolemera!”’
-