Yeremiya 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani Yeremiya?” Ndipo ine ndinayankha kuti: “Ndikuona nkhuyu. Nkhuyu zabwino, nʼzabwino kwambiri koma nkhuyu zoipa, nʼzoipa kwambiri. Ndi zoipa kwambiri moti munthu sangadye.”+
3 Kenako Yehova anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani Yeremiya?” Ndipo ine ndinayankha kuti: “Ndikuona nkhuyu. Nkhuyu zabwino, nʼzabwino kwambiri koma nkhuyu zoipa, nʼzoipa kwambiri. Ndi zoipa kwambiri moti munthu sangadye.”+