-
Yeremiya 25:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mawu anga onse amene ndanena okhudza zimene ndidzachitire dzikolo ndidzawakwaniritsa. Ndidzakwaniritsa zonse zimene zalembedwa mʼbuku ili, zimene Yeremiya wanenera kuti zidzachitikira mitundu yonse.
-