Yeremiya 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 mafumu onse akumpoto, akutali ndi apafupi, mmodzi ndi mmodzi ndipo ndinamwetsanso maufumu ena onse apadziko lapansi. Koma mfumu ya Sesaki*+ idzamwa pambuyo pa onsewa. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:26 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 20-21
26 mafumu onse akumpoto, akutali ndi apafupi, mmodzi ndi mmodzi ndipo ndinamwetsanso maufumu ena onse apadziko lapansi. Koma mfumu ya Sesaki*+ idzamwa pambuyo pa onsewa.