-
Yeremiya 25:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Tamverani! Abusa akufuula
Komanso anthu olemekezeka pa gulu la nkhosa akulira.
Chifukwa Yehova akuwononga malo awo odyetserako ziweto.
-