Yeremiya 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iye watuluka mʼmalo ake okhalamo ngati mkango wamphamvu,*+Dziko lawo lakhala chinthu chochititsa mantha.Chifukwa cha lupanga lake lankhanzaKomanso chifukwa cha mkwiyo wake woyaka moto.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:38 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 23
38 Iye watuluka mʼmalo ake okhalamo ngati mkango wamphamvu,*+Dziko lawo lakhala chinthu chochititsa mantha.Chifukwa cha lupanga lake lankhanzaKomanso chifukwa cha mkwiyo wake woyaka moto.”