Yeremiya 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ansembe, aneneri ndi anthu onse anamva Yeremiya akulankhula mawu amenewa mʼnyumba ya Yehova.+
7 Choncho ansembe, aneneri ndi anthu onse anamva Yeremiya akulankhula mawu amenewa mʼnyumba ya Yehova.+