-
Yeremiya 26:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako akalonga ndi anthu onse anauza ansembe ndi aneneri kuti: “Munthu uyu sakuyenera kuphedwa chifukwa walankhula nafe mʼdzina la Yehova Mulungu wathu.”
-