Yeremiya 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Panalinso munthu wina amene ankanenera mʼdzina la Yehova. Iyeyu anali Uliya mwana wa Semaya wa ku Kiriyati-yearimu.+ Iye ananeneratu zimene zidzachitikire mzindawu mofanana ndi mawu a Yeremiya.
20 Panalinso munthu wina amene ankanenera mʼdzina la Yehova. Iyeyu anali Uliya mwana wa Semaya wa ku Kiriyati-yearimu.+ Iye ananeneratu zimene zidzachitikire mzindawu mofanana ndi mawu a Yeremiya.