Yeremiya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Mfumu Yehoyakimu,+ asilikali ake onse amphamvu ndi akalonga onse anamva mawu amene Uliya ananena. Zitatero mfumu inakonza zoti imuphe.+ Uliya atamva zimenezo, nthawi yomweyo anachita mantha ndipo anathawira ku Iguputo.
21 Ndiyeno Mfumu Yehoyakimu,+ asilikali ake onse amphamvu ndi akalonga onse anamva mawu amene Uliya ananena. Zitatero mfumu inakonza zoti imuphe.+ Uliya atamva zimenezo, nthawi yomweyo anachita mantha ndipo anathawira ku Iguputo.