-
Yeremiya 27:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Chifukwa anthu amenewa akulosera zabodza kwa inu, mukawamvera mudzatengedwa mʼdziko lanu nʼkupita dziko lakutali ndipo ine ndidzakubalalitsani moti mudzawonongedwa.
-