Yeremiya 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mfumu Zedekiya+ ya ku Yuda ndinaiuzanso mawu amenewa kuti: “Ikani makosi anu mʼgoli la mfumu ya Babulo nʼkuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake kuti mukhalebe ndi moyo.+
12 Mfumu Zedekiya+ ya ku Yuda ndinaiuzanso mawu amenewa kuti: “Ikani makosi anu mʼgoli la mfumu ya Babulo nʼkuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake kuti mukhalebe ndi moyo.+