Yeremiya 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musawamvere. Tumikirani mfumu ya Babulo kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+ Kodi mzindawu ukhale bwinja chifukwa chiyani?
17 Musawamvere. Tumikirani mfumu ya Babulo kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+ Kodi mzindawu ukhale bwinja chifukwa chiyani?