-
Yeremiya 27:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma ngati iwo ndi aneneri ndipo akulankhula mawu a Yehova, iwo apemphe kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba kuti ziwiya zimene zinatsala mʼnyumba ya Yehova, mʼnyumba ya mfumu ya Yuda ndi zimene zinatsala ku Yerusalemu zisatengedwe kupita ku Babulo.’
-