Yeremiya 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Aneneri akalekale amene analipo ineyo ndisanakhalepo komanso iweyo usanakhalepo ankalosera za nkhondo, masoka ndi miliri yoti igwere* mayiko ambiri ndi maufumu amphamvu.
8 Aneneri akalekale amene analipo ineyo ndisanakhalepo komanso iweyo usanakhalepo ankalosera za nkhondo, masoka ndi miliri yoti igwere* mayiko ambiri ndi maufumu amphamvu.