-
Yeremiya 30:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mtsogoleri wake adzachokera pakati pa anthu ake,
Ndipo wolamulira wake adzachokera pakati pa mbadwa zake.
Ndidzamulola kuti andiyandikire ndipo adzabwera kwa ine.
Chifukwa ndi ndani amene angalimbe mtima kuti andiyandikire?” akutero Yehova.
-