-
Yeremiya 31:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Yehova wanena kuti:
“Anthu amene anapulumuka ku lupanga, ndinawakomera mtima mʼchipululu,
Pamene Isiraeli ankapita kumalo ake opumulirako.”
-