Yeremiya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anaonekera kwa ine ali kutali ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale. Nʼchifukwa chake ndakukokera kwa ine ndi chikondi chokhulupirika.*+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:3 Yeremiya, ptsa. 143-144
3 Yehova anaonekera kwa ine ali kutali ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale. Nʼchifukwa chake ndakukokera kwa ine ndi chikondi chokhulupirika.*+