Yeremiya 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Udzadzalanso mpesa kumapiri a ku Samariya.+Anthu adzadzala mpesa nʼkudya zipatso zake.+