Yeremiya 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wanena kuti: “Fuulirani Yakobo mosangalala, Fuulani mosangalala chifukwa muli patsogolo pa mitundu ina.+ Lengezani zimenezi. Tamandani Mulungu nʼkunena kuti,‘Inu Yehova pulumutsani anthu anu, otsalira a Isiraeli.’+
7 Yehova wanena kuti: “Fuulirani Yakobo mosangalala, Fuulani mosangalala chifukwa muli patsogolo pa mitundu ina.+ Lengezani zimenezi. Tamandani Mulungu nʼkunena kuti,‘Inu Yehova pulumutsani anthu anu, otsalira a Isiraeli.’+