Yeremiya 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wanena kuti: “‘Tonthola, usalire ndipo usagwetsenso misozi,Chifukwa ulandira mphoto pa ntchito yako,’ akutero Yehova. ‘Ana ako adzabwerera kuchokera kudziko la mdani.’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:16 Nsanja ya Olonda,12/15/2014, tsa. 21
16 Yehova wanena kuti: “‘Tonthola, usalire ndipo usagwetsenso misozi,Chifukwa ulandira mphoto pa ntchito yako,’ akutero Yehova. ‘Ana ako adzabwerera kuchokera kudziko la mdani.’+