Yeremiya 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+Mutandithandiza kuzindikira, ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni. Ndinachita manyazi ndipo ndinaoneka wonyozeka,+Chifukwa cha zinthu zimene ndinachita ndili wachinyamata.’” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:19 Nsanja ya Olonda,4/1/2012, tsa. 11
19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+Mutandithandiza kuzindikira, ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni. Ndinachita manyazi ndipo ndinaoneka wonyozeka,+Chifukwa cha zinthu zimene ndinachita ndili wachinyamata.’”