Yeremiya 31:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Yehova wanena kuti: “‘Ngati kumwamba kungayezedwe ndipo ngati maziko a dziko lapansi angafufuzidwe, ndiye kuti inenso ndingakane mbadwa zonse za Isiraeli chifukwa cha zonse zimene achita,’ akutero Yehova.”+
37 Yehova wanena kuti: “‘Ngati kumwamba kungayezedwe ndipo ngati maziko a dziko lapansi angafufuzidwe, ndiye kuti inenso ndingakane mbadwa zonse za Isiraeli chifukwa cha zonse zimene achita,’ akutero Yehova.”+