Yeremiya 31:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chigwa chonse cha mitembo ndi cha phulusa,* masitepe onse mpaka kukafika kuchigwa cha Kidironi,+ mpaka kukona ya Geti la Hatchi+ chakumʼmawa, zidzakhala zoyera kwa Yehova.+ Mzindawu sudzazulidwa ndipo sudzagwetsedwanso.”
40 Chigwa chonse cha mitembo ndi cha phulusa,* masitepe onse mpaka kukafika kuchigwa cha Kidironi,+ mpaka kukona ya Geti la Hatchi+ chakumʼmawa, zidzakhala zoyera kwa Yehova.+ Mzindawu sudzazulidwa ndipo sudzagwetsedwanso.”