Yeremiya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya mʼchaka cha 10 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda. Chimenechi chinali chaka cha 18 cha Nebukadinezara.*+
32 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya mʼchaka cha 10 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda. Chimenechi chinali chaka cha 18 cha Nebukadinezara.*+