Yeremiya 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka mʼmanja mwa Akasidi, chifukwa adzaperekedwa ndithu mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzalankhulana ndi kuonana naye maso ndi maso.”’+
4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka mʼmanja mwa Akasidi, chifukwa adzaperekedwa ndithu mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzalankhulana ndi kuonana naye maso ndi maso.”’+