Yeremiya 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Kukubwera Hanameli mwana wa Salumu mʼbale wawo wa bambo ako, kudzakuuza kuti: “Ugule munda wanga wa ku Anatoti+ chifukwa munthu woyamba amene ali ndi ufulu wogula mundawo ndi iweyo.”’”+
7 ‘Kukubwera Hanameli mwana wa Salumu mʼbale wawo wa bambo ako, kudzakuuza kuti: “Ugule munda wanga wa ku Anatoti+ chifukwa munthu woyamba amene ali ndi ufulu wogula mundawo ndi iweyo.”’”+