-
Yeremiya 32:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Hanameli mwana wa mʼbale wawo wa bambo anga anandipeza mʼBwalo la Alonda mogwirizana ndi zimene Yehova ananena. Iye anandiuza kuti: “Gula munda wanga wa ku Anatoti, umene uli mʼdziko la Benjamini, chifukwa iweyo ndi amene uli ndi ufulu wouwombola nʼkuutenga kuti ukhale cholowa chako. Uugule kuti ukhale wako.” Atatero ndinazindikira kuti mawu amenewa anali a Yehova.
-