Yeremiya 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndinagula munda wa Hanameli mwana wa mʼbale wawo wa bambo anga umene unali ku Anatoti. Ndinamuyezera ndalama+ zake ndipo zinakwana masekeli* 7 ndi ndalama zina 10 zasiliva.
9 Choncho ndinagula munda wa Hanameli mwana wa mʼbale wawo wa bambo anga umene unali ku Anatoti. Ndinamuyezera ndalama+ zake ndipo zinakwana masekeli* 7 ndi ndalama zina 10 zasiliva.