-
Yeremiya 32:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Tenga makalata awa, makalata a pangano ogulira mundawa, kalata yomata ndi kalata yosamatayo ndipo uwaike mʼmbiya kuti akhale kwa nthawi yaitali.’
-