Yeremiya 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli mʼdziko la Iguputo pogwiritsa ntchito zizindikiro, zodabwitsa, dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+
21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli mʼdziko la Iguputo pogwiritsa ntchito zizindikiro, zodabwitsa, dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+