Yeremiya 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo analowa mʼdzikoli nʼkulitenga kuti likhale lawo, koma sanamvere mawu anu kapena kuyenda motsatira malamulo anu. Iwo sanachite zinthu zonse zimene munawalamula kuti achite, nʼchifukwa chake munawagwetsera masoka onsewa.+
23 Iwo analowa mʼdzikoli nʼkulitenga kuti likhale lawo, koma sanamvere mawu anu kapena kuyenda motsatira malamulo anu. Iwo sanachite zinthu zonse zimene munawalamula kuti achite, nʼchifukwa chake munawagwetsera masoka onsewa.+