-
Yeremiya 32:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Choncho ponena za mzinda uwu umene mukunena kuti uperekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Babulo kuti uwonongedwe ndi lupanga, njala ndi mliri, Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti,
-