-
Yeremiya 33:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Yehova amene anapanga dziko lapansi, Yehova amene anawumba dzikoli nʼkulikhazikitsa mwamphamvu, Mulungu amene dzina lake ndi Yehova, wanena kuti,
-