Yeremiya 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawayeretsa ku zolakwa zonse zimene anandichimwira+ ndipo ndidzawakhululukira zolakwa zawo zonse zimene anandichimwira nʼkuphwanya nazo malamulo anga.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:8 Yeremiya, ptsa. 152-153
8 Ndidzawayeretsa ku zolakwa zonse zimene anandichimwira+ ndipo ndidzawakhululukira zolakwa zawo zonse zimene anandichimwira nʼkuphwanya nazo malamulo anga.+