-
Yeremiya 33:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 “Yehova wanena kuti: ‘Pamalo ano amene mudzanene kuti ndi bwinja, opanda anthu kapena ziweto, mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu imene yawonongeka, moti mulibe anthu ndipo simukukhala aliyense ngakhale ziweto, mʼmalo amenewa mudzamveka
-