Yeremiya 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Taonani! Masiku akubwera pamene ndidzakwaniritsa lonjezo langa labwino lokhudza nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda,’ akutero Yehova.+
14 “‘Taonani! Masiku akubwera pamene ndidzakwaniritsa lonjezo langa labwino lokhudza nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda,’ akutero Yehova.+