Yeremiya 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova wanena kuti, ‘Mʼnyumba ya Davide simudzalephera kupezeka munthu woti akhale pampando wachifumu wa nyumba ya Isiraeli.+
17 “Yehova wanena kuti, ‘Mʼnyumba ya Davide simudzalephera kupezeka munthu woti akhale pampando wachifumu wa nyumba ya Isiraeli.+