Yeremiya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzachulukitsa mbadwa* za Davide mtumiki wanga ndi Alevi amene akunditumikira. Ndidzazichulukitsa mofanana ndi kuchuluka kwa nyenyezi zonse zakumwamba* zimene sizingawerengedwe ndiponso mofanana ndi mchenga umene sungayezedwe.’”
22 Ine ndidzachulukitsa mbadwa* za Davide mtumiki wanga ndi Alevi amene akunditumikira. Ndidzazichulukitsa mofanana ndi kuchuluka kwa nyenyezi zonse zakumwamba* zimene sizingawerengedwe ndiponso mofanana ndi mchenga umene sungayezedwe.’”